THE HOME MANAGERS
POSITION: HOUSE MAID
Onse osangalatsidwa alembe ndi kutumiza ma kalata awo komanso chithunzi chawo ku nambala iyi; 0995 499 833.
Close of Business: 28.10.25
POSITION: HOUSE MAID
Onse osangalatsidwa alembe ndi kutumiza ma kalata awo komanso chithunzi chawo ku nambala iyi; 0995 499 833.
MAIDS WANTED IN THREE CATEGORIES/ Azimayi a ntchito ya Mnyumba akufunidwa mwachangu mu zigawo izi;
1) Pakufunika azimayi a ntchito ya Mnyumba wogonela konko, ku Blantyre komanso Lilongwe. Akhale woti amatha kuphika bwino kwambiri komanso oti anagwilapo kale yolera ana komanso ya Mnyumba, komanso odziwa cleaning komanso kuchapa ndi kusita. A Seventh Day komanso amipingo yopemphela Sunday Ali olimbikitsika kulembela ntchito yimeneyi.
2) Pakufunika azimayi ogwila ntchito ya Mnyumba komanso kusamala ana koma yoyendela mu mzinda wa Blantyre. Akhale woti amapemphela Saturday or Sunday komanso amadela ozungulira New Naperi.
3) Pakufunika azimayi a ntchito ya Mnyumba wogonela konko koma akhale woti Ali ndi experience ya zaka zopitilira zitatu pantchito. Akhale woti Ali ndi ma Reference woti anawalembela komwe ankagwila kale.
NB: Onse osangalatsidwa alembe ndi kutumiza ma kalata awo komanso chithunzi chawo ku nambala iyi; 0995 499 833.
NB: Akhale azimayi osachepela zaka 30 komanso osapitilira zaka 50.
Azimayi okhawo amene azakhale ndi zoziyeneleza pantchitoyi ndi amene azatengedwe komanso kuyimbilidwa phone.
NB: Ma salary ndi abwino ovomelezeka ndi Boma. Komanso kwa mabwana abwino.
Closing date: 28th October 2025.
Comments
Post a Comment